Dzikilani

Gospel Tract and Bible Society ipereka mabuku a Uthenga Wabwino aulere kuti azigwiritsidwa ntchito pophunzira ndi kugawira kuti athandize kufalitsa Uthenga Wabwino. Timapereka mabuku pamitu yosiyanasiyana komanso m’zinenero zopitilira 80.