Moyo Wosokoneka

Nthawi ino muli ndi moyo;mukupuma;mukudya ndi kumwa madzi tsiku ndi tsiku; mukutha kuyendayendakugwira ntchito zanu ndi kumagona. Mwina mukukhala moyo wokandwa mwina wodandaula chifukwa cha mabvuto. Tsiku ndi tsiku dzuŵa likutuluka ndipo likuloŵa; ku malo ena mwana akubadwa, komanso kumalo ena wina akumwalira. PAMENEPA TIONA KUTI ZONSE ZA MOYO WAPANSI PANO NDI ZOSAKHALITSA. KOMA, NDIKADZAFA NDIDZAPITA KUTI? Kaya ndine Mkhristu wofooka kapena wopembedza ku Chisilamu kapena wopembedza ku Chibuda kapena wopembedza ku Chiyuda kapena wopembedza mizimu ya makolo kapena wopembedza chimodzi cha zipembezo zambiri zimene tingazitchule, kapena wosapembedza kumene –

Amharic Arabic Bengali Chinese English French Haitian Creole Hindi Indonesian Italian Japanese Kazakh Korean Lingala Nepali (Macrolanguage) Oromo Persian Polish Portuguese Punjabi Russian Southern Sotho Spanish Swedish Tajik Tamil Thai Turkish Ukrainian Urdu Vietnamese

March 27, 2019 in  Moyo Wosokoneka, Mphamvu 3 minutes