Chikondwelero

“Mtendere, uli kuti mtendere - wa maiko athu, m’nyumba zathu, makamaka mtendere wa mitima yathu? Kulira kowawitsa moyo uku kulilira mtendere ktwakhala kuli kumvekabe pakati pa mibadwo yonse; komatu kuliraku nthawi zones kukukulira kulira chifukwa cha kuchuluka zochitika padziko zimene zikupangitsa kuti mtendere usowekedi. M’bale ukuwerengawe, kulira kwa mtima wako ndi kumenekunso kodi? Mkati mwa zosowetsa mtendere ndi zosakhutitsa mtima zonse, kodi umalakalakadi utapeza mtendere wamumtima umene uli opambana zonse?

Amharic Arabic Bemba (Zambia) Bengali Burmese Chinese Dutch English French German Haitian Creole Indonesian Japanese Kazakh Kinyarwanda Korean Lingala Malagasy Mongolian Mossi Nepali (Macrolanguage) Norwegian Oromo Persian Plautdietsch Portuguese Punjabi Romanian Rundi Russian Southern Sotho Spanish Swedish Tagalog Tajik Telugu Thai Tonga (Zambia) Turkish Ukrainian Urdu

August 3, 2023 in  Chikondwelero 9 minutes